Desperate chords with lyrics by Faith Mussa - Easy chords and tabs for guitar

Faith Mussa – Desperate chords

Chords:
Transpose:
DESPERATE
Written by : Faith Mussa
Composed by: Faith Mussa
Guitar by Faith Mussa

Key of D#. Cappo placed on 3rd fret


Intro
C Am Fmaj7 G
C Am Fmaj7 G

C DmIne ndili desperate for your Love
F GIne ndili desperate for your hand
C Am Ine ndili desperate for your touch
F G CIne ndili desperate, deperate for You
Verse 1
Am F G Chilichonse chomwe ndili nacho chachokera kwa inu
C Am F G Ngakhale ntchito yomwe tikugwirayi timayamika inu
C Am F GSukulu yonse yomwe taphunzirayi timayamika inu
C Am F G Ngakhale magitala tikuimbawa timayamika inu
Ine ndili desperate for your Love Ine ndili desperate for your hand Ine ndili desperate for your touch Ine ndili desperate, x2 Chorus Ine ndili desperate Ndili desperate Ine ndili desperate Ndili desperate Ine ndili desperate, ndili desperate, ndili desperate, Ine ndili desperate, ndili desperate, ndili desperate, Verse2 Chilichonse chomwe ndidzachite ndidzatumikira inu Ngakhale nyimbo zomwe ndidzaimbe, ndidzaimbira inu Mtim wanga thupi langa zones, zidzatumikira inu Ndikufuna mbuye mukamandiona, mudzingomwetulira Ine ndili desperate for your Love Ine ndili desperate for your hand Ine ndili desperate for your touch Ine ndili desperate, x2 Chorus Ine ndili desperate Ndili desperate Ine ndili desperate Ndili desperate Ine ndili desperate, ndili desperate, ndili desperate, Ine ndili desperate, ndili desperate, ndili desperate, Bridge
C AmNthawi zonse ndimafuna,
F Kuyenda nanu
GChikondi chanu chinazula
C Mtima wanga
Am F G Mukandiona ndikukwera phiri, kukapemphera, ndili desperate
C AmNgakhale ndimayenda
F Mnthunzi wa imfa
G CSindidzaopa poti mbuye, Mulinane
Am FChibonga chanu n’ndodo yanu zindisangalatsa,
Ine ndili desperate for your Love Ine ndili desperate for your hand Ine ndili desperate for your touch Ine ndili desperate, desperate for you! For you, for you Ndili desperate for you For you, for you Ine ndili desperate for you For you, for you ending Ndikufuna Nkhope yanu Mbuye, Ndikufuna nkono chanu Mbuye Ndikufuna dzanja lanu mbuye, Edipo ndili desperate, Ndikufuna zozizwa zanu mbuye, Ndikufuna chiyero chanu mbuye Ndikufuna dzanja lanu mbuye, Edipo ndili desperate, Desperate for you
Please rate this tab:
x1.0